Ulendo wa ku joni

Ulendo wa ku joni Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ulendo wa ku joni, Travel and transport, Malawi, Johannesburg.

26/11/2024

Assalam Alaikum Warahmatullah wabarakatuh
Mwadzuka bwanji Mabwana ndi Madona?
Ndili munjira waku DURBAN,, Chonde anthu Aku DURBAN sungani nthawi Malo omwe tagwirizana kuzakumana ndikupatseni Katundu wanu.
Ku DURBAN ndikhala mpaka Saturday In Shaa Allah,choncho Kwa omwe muli ndikatundu m***a kundiuza before Saturday.
Ulendo obwelera Ku Malawi uzakhala pa 4 December Lachitatu week yamawa In Shaa Allah.
Zikomo kwambiri

21/11/2024

Muli bwanji ma bwana nonse,.??
Ulendo wa ku Jobek ulipo Lowelukali Ma ticket ndi odzadza koma katundu bweletsani ndithu malo alipo.
Osaiwala konyamukila ndi komwekuja kumangochi ...

Kwa amene muli kuja ku SouthAfrica.. khonzekani chifukwa ma ticket tiyamba kudula pa 25 November ndipo ulendo ndi wa Pa 4 December... Tipasileni katundu tikasiye kumudzi ..ngakhale mutayikamo Bread akafika ali wa fresh nankha si tiyenda masiku ochepa.....

Zikomo mabwana
Number ndi yomwe ina 0715492470

27/10/2024

Kungokumbusana....Ulendo wathu ..timachoka Johannesburg kupita Mangochi...Timayenda Lachitatu lililonse kuchoka ku Jobek to Mangochi
Komanso Loweluka lililonse kuchoka ku MANGOCHI. Kupita ku Joni..
Number ndi yomwe ija.+27715492470..
Amene mumandiyimbira..tikumane mawa pa office ku jobek (75Goud street)
Zikomo kwambiri..

24/10/2024
22/10/2024

Ulendo ulipo pa 30 pano...kubwelera ku Malawi....kenako pa 9 nkubwera ku South Africa..
Amene muli ndikatundu bweresani ndithu..pano tili ku Durban kutolera katundu
*13 November* kuchoka Ku South Africa kubwelera Ku Malawi.

In Shaa Allah

19/10/2024

Mwaswera bwanji mabwana ndi madona.
Timanyamula katundu opita ku Malawi komanso ku South Africa.
Timatenganso anthu kuchoka ku Malawi komanso kuchoka ku South Africa.
Ulendo wathu ndi wa Bus. Ndipo timayenda masiku awiri.
Timayenda Loweluka kuchoka ku MANGOCHI. ndipo Lachitatu kuchoka kuja ku South Africa.
Ofuna kutumiza katundu.. atipeze pa number iyi..0027715492470 pa Whatsapp.

Zikomo kwambiri..

.................

Address

Malawi
Johannesburg

Telephone

+27765492470

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ulendo wa ku joni posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share