31/07/2026
Mwadzuka bwanji chonde mukafunsa Za mtengo imakhala mitengo ya ticket only Ife sitingalembe zamnsewu tisakudziwa Za Vuto lanu mu passport chonde tiyeni tikapatsidwa mitengo tionetsetse Kuti tikumafunsa zomwe pa list palibepo chonde chonde timakhala tikukanika kuthandizaso ena Ngati tikhalire kuyankha munthu mmodzi
Pomaliza tiyeni tichepetse ma voice note kapena ma audio chifukwa nthawi zambiri tikakhala pa call sitingayankhe or kumvera simple lembani message or call poti timakhala tikulandira so many calls tiyeni Ngati sitinayankhe lembani message please