Lonje Logistics Mw

Lonje Logistics Mw TIKAMATI MUNTHU WAGULA GALIMOTO TIMAKAMBA YOITANITSA . Pamitengo Yachimalawi

Welcome to our page Lonje logistics Mw since 2021
We help people importing CARS From Japan, We also Clear And Deliver to your destination
We are looking forward to save you with high quality service NDIBWINO MUNTHU KUDEKHA KWA MIYEZI IWIRI OR ITATU MKUPEZA CHINTHU CHOTI UKHALA NACHO ZAKA ZAMBIRI KUSINAYA NDIKUPEZA CHINTHU SAME DAY MKUMAZUNZIKA NACHO KWA ZAKA(Stress yogona panseu simasewera)
CALL

OR WHATSAPP ⁨0881 13 05 52⁩
IFE: Timathandiza discount
-Kuwelengesera
-Kuwunikira Ubwino wa galimoto mukufuna Komanso kupanga deliver pakhomo pano .

IMPORTED,  CLEARED AND DELIVERED BY YOUR OWN Lonje Logistics Mw  17 june 2026For inquiry WhatsApp +265881130552Ife timau...
17/06/2026

IMPORTED, CLEARED AND DELIVERED BY YOUR OWN Lonje Logistics Mw 17 june 2026
For inquiry WhatsApp +265881130552
Ife timaunikira ubwino wa galimoto musanagule komanso kuwelengera ma cost mwaulele
Komaso ma service athu ndi a ulele kwa onse anadusa Zaka 90 zakubadwa..
Good Morning Everyone

Mu nyengo ya ma deliveries ochuluka zedi ..Ifetu timanyadira ma customer athu nonse mumatipasa ganyu .kamba Koti ku Mala...
11/06/2026

Mu nyengo ya ma deliveries ochuluka zedi ..
Ifetu timanyadira ma customer athu nonse mumatipasa ganyu .kamba Koti ku Malawi kuno anyamata aganyu tilipo ochuluka..ndichifukwa chakeso nafe sitifooka ngakhale ma forex ndi zina zikutisowetsa mtendele..
Ganyu wathu ndiyemwe uja
KUITANITSA
KUPANGA CLEAR
KUPANGA DELIVERIES. Ma galimoto omwe akuchoka ku japan
WhatsApp +265881130552

NTCHITO YOTHYAKUKA LERO PA 4 JUNE 2026 IMPORTED AND CLEARED BY US NDE TIKUBWERA NDI MA DELIVERIES ANYOOOO!!WHATSAPP +265...
04/06/2026

NTCHITO YOTHYAKUKA LERO PA 4 JUNE 2026
IMPORTED AND CLEARED BY US
NDE TIKUBWERA NDI MA DELIVERIES ANYOOOO!!
WHATSAPP +265881130552 FOR INQUIRY

18/05/2026
The design was made by our top fan for free as one way of showing love and support. You can also get your graphics by co...
18/05/2026

The design was made by our top fan for free as one way of showing love and support. You can also get your graphics by contacting him on +265 995 27 99 10 follow MACRE Graphics

Congratulations to our happy customer charity banda . thanks for trusting Lonje logistics 🔥🔥Whatsapp 0881130552 for vehi...
23/04/2026

Congratulations to our happy customer charity banda . thanks for trusting Lonje logistics 🔥🔥
Whatsapp 0881130552 for vehicle import , Clearing and Delivery

Imported by SBT Discounted Vehicle Agency Delivered By   on 22 April 2026 Whatsapp+265881130552 For Vehicle Import , Cle...
22/04/2026

Imported by SBT Discounted Vehicle Agency Delivered By on 22 April 2026
Whatsapp+265881130552 For Vehicle Import , Clearance And Delivery

Address

Area 3
Lilongwe
265

Telephone

+265881130552

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lonje Logistics Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Lonje Logistics Mw:

Share