Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe

Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe, Balaka.

Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe.ili ndi gulu lathu lomwe lili pa whatsapp. Kutengera ndi makhalidwe ...
10/02/2024

Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe.

ili ndi gulu lathu lomwe lili pa whatsapp. Kutengera ndi makhalidwe a zamakonozi zomwe ma # pa whatsapp amapezeka apangidwa Ban mosayembekezera kuti mupezenso link ina olo anzanu kuti atipeze mosavuta page ino izithandizira njira imeneyo.

Kwama member a sopano omwe mwangopanga like page ino kumene ku group limeneli anzanu amapezako thandizo la zovuta zina za mthupi, komanso kupanga save transport. Thandizo lake ndi monga mankhwala a MwanaMphepo, Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe, Amauka, Ama 11, Obwenza ndata, Alikango komanso omwe muthakuwagulira abambo monga Gondolosi ngati mwagwilizana.

Thandizo limeneli timatumiza kulikonse mukafuna kudziwa zambiri pa tsamba limeneli tipezeni ku inbox tikutumizireni link yapa whatsapp pomwe muzikatha kufunsa mafunso momasuka, kuyankhulana ndi Admin momasuka komanso muzikawonanso ma umboni a anzanu.

Chidziwitso: Pasapezeke wina aliyense wokulowelani ku inbox kugwilizana nanu zomwe zakambidwa pa tsamba lino kuti ndi modzi mwathu kuti mugwilizane naye. Kwama member akale kuti musimikize kuti tsamba lino simunasochele ndipezeni ku Whatsapp group Admin ndiloweleni ku inbox kuti ndikusimikizireni.

Address

Balaka

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tichedze Azimayi za Tseketseke wa Lilime la Ng'ombe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share