30/07/2026
PUBLIC NOTICE: LOST NATIONAL REGISTRATION CARDS - NRC
Hello Valued Customers of KOBS TRANSPORTERS LIMITED
Zambia - Malawi Buses
This is to inform our passengers that we have found some National Registration Cards (NRCs) 🪪 that were left/lost on our buses.
If you have traveled with us and lost your NRC, kindly:
1. Go through the pictures posted on this page to check if your NRC is among those found.
2. Come and collect your NRC at our Lusaka Office from the Safety Management Office.
Please bring proof of identification when collecting.
Thank you for traveling with KOBS TRANSPORTERS LIMITED.
Your safety and property matter to us.
Management
KOBS TRANSPORTERS LIMITED_
Lusaka, Zambia
(Nyanja version)
CHIDZIWITSO KWA ANTHU: Makhadi Otayika a NRC
Moni kwa Makasitomala Onse a KOBS TRANSPORTERS LIMITED
Magalimoto ochokera Zambia kupita ku Malawi
Tikudziwitsa anthu onse omwe ayenda nafe kuti tapeza Makhadi a NRC 🪪 omwe anasiyidwa/tayika m'mabasi athu.
Ngati mwayenda nafe ndipo mwataya NRC yanu, chonde:
1. Yang'anani zithunzi zomwe tatumiza pa page iyi kuti muone ngati NRC yanu ilipo.
2. Bwerani kudzatenga NRC yanu pa Ofesi yathu ya Lusaka ku Office ya Safety Management.
Mukabwera kutenga, chonde bwerani ndi chizindikiritso china.
Zikomo chifukwa choyenda nafe KOBS TRANSPORTERS LIMITED.
Chitetezo chanu ndi katundu wanu ndizofunika kwa ife.
Utsogoleri
KOBS TRANSPORTERS LIMITED
Lusaka, Zambia