Golden Logistics

Golden Logistics Tumizani katundu kumalawi mosavuta, modalilika komanso mwachangu

GOLDEN LOGISTICS MALAWI
+27 69 420 8828
(1)

27/01/2026
🔥Nkhaniyi ndiyosavuta, ndiyasimple basi. 📲Titchayileni lamya pa +27694208828. Zikatero tibwera tidzanyamula katundu koma...
27/01/2026

🔥Nkhaniyi ndiyosavuta, ndiyasimple basi.

📲Titchayileni lamya pa +27694208828. Zikatero tibwera tidzanyamula katundu komanso kukasiya patkhomo.

🔥Golden Logistics ndi kampani yokhayo yodalirika pakatumizidwe ka katundu kuchokera ku South Africa kupita ku Malawi. 💯U...
26/01/2026

🔥Golden Logistics ndi kampani yokhayo yodalirika pakatumizidwe ka katundu kuchokera ku South Africa kupita ku Malawi.

💯Ukadaulo wathu wakhala waphindu kwa ma kampani, anthu ochita malonda komanso ndi wina aliyense amene akufuna kutumiza katundu wawo mwachangu, motetezeka komanso modalirika.

🎯Anthu onse ochita malonda komanso makampani amapindula ndi mitengo yathu yotsika potumiza katundu wawo pa mtendo wa R6/kg ndi ndondomeko ya Office to Office, pamene anthu ena onse amapindula podzera kuti katundu wawo amadzatengedwa kuchokera pakhomo pomwe akutumizira komanso ku Malawi amakasiyidwa pakhomo pomwe katunduyo akutumizidwa ndi ndondomeko yathu ya Door to Door.

📲Ngati mukufuna kumva zambiri chezani nafe kudzera pa whatsapp +27694208828

🔥💯Kutumiza katundu ku Malawi from South africa kwaphweka!!!✅Akulu akulu, zabwino zipose apa!!✅
23/01/2026

🔥💯Kutumiza katundu ku Malawi from South africa kwaphweka!!!

✅Akulu akulu, zabwino zipose apa!!✅

🔥Chimangofunika ndi changu poti malo nde masiku ano akumatha mwachangu. 👌Chosangalatsa ndichakuti maulenso anthu amakhal...
21/01/2026

🔥Chimangofunika ndi changu poti malo nde masiku ano akumatha mwachangu.

👌Chosangalatsa ndichakuti maulenso anthu amakhalanso a machawi poonetsatsetsa kuti katundu wanu wakafika munthawi yake mwachangu komanso motetezeka.

📲Ngati mukufuna kumva zambiri tiyankhuleni pa whatsapp +27694208828.

🔥Affordable prices! Great savings!!🔥🎯Our OFFICE TO OFFICE services allows all people, bussinesses, companies and transpo...
21/01/2026

🔥Affordable prices! Great savings!!🔥

🎯Our OFFICE TO OFFICE services allows all people, bussinesses, companies and transporters sending in bulk to pay a standard price of R6/kg from Johannesburg to Malawi.
With this service your parcels are to be dropped at and collected from our warehouses.

🎯With DOOR TO DOOR services give our customers a convenience of sending their parcels from the comfort of their homes and parcels being dropped at the exact location they are being sent.

📲For more information, kindly contact us on +27694208828.

💯Happy customer kujambulitsa pa gate ya office yathu ku Johannesburg. 📍Nanu mukhoza kutibweretsera Katundu wanu ku 76 en...
18/01/2026

💯Happy customer kujambulitsa pa gate ya office yathu ku Johannesburg.

📍Nanu mukhoza kutibweretsera Katundu wanu ku 76 end street doornfontein, Johannesburg, south Africa

✅Timabweranso pakhomo panu kudzaatenga katuduyo komanso kukausiyirani pakhomo pawo pa omwe mukuwatumizira katunduyo.

📲Mukufuna kumva zambiri tiyankhuleni kudzera pa WhatsApp +27694208828

🚛Tikhale tikunyamuka posachedwapa ndipo yesetsanibkupeza Malo a Katundu wanu mwamsanga.

🎯Kwa anthu onse ochita malonda ndipo mumatumiza katundu wanu kuchokera ku south africa kupita ku malawi, tsopano muli nd...
16/01/2026

🎯Kwa anthu onse ochita malonda ndipo mumatumiza katundu wanu kuchokera ku south africa kupita ku malawi, tsopano muli ndi mwayi otumiza katundu wanu mwachangu ndi Golden Logistics.

👌Tsopano ma truck athu amayenda week iliyonse kuchokera ku SA kupita ku Malawi. Izi zikupereka mwayi oti tsopano m***a kutumiza malonda anu sabata iliyonse.

📲Tiyankhuleni kudzera pa whatsapp +27694208828

🚨🚨Joburg Joburg Joburg!!!!🚨🚨🚛Tili mkati motolera Katundu mumzinda wa Johannesburg. Magalimoto athu akuzungulira mumzinda...
14/01/2026

🚨🚨Joburg Joburg Joburg!!!!🚨🚨

🚛Tili mkati motolera Katundu mumzinda wa Johannesburg. Magalimoto athu akuzungulira mumzindawu komanso ndi Madera onse oyandikira kumeneko, kutolera Katundu wa amene akufuna kutumiza ku Malawi.

📲Kutumiza Katundu ndi Golden Logistics ndikosavuta. Tiyankhuleni kudzera pa WhatsApp +27694208828, zikatero ndekuti tigwirizana tsiku ndi nthawi yoti tifike pakhomo panu kudzaatenga katuduyo.

💯Golden Logistics. Transport ndi yemweyu basi
GINTE

Address

76 End Street
Doornfontein
2028

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Golden Logistics posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Golden Logistics:

Share