Bye Bye Bus Company

Bye Bye Bus Company Bye Bye Coaches Company ndiyomwe ingakuendesen bwino kuchok ku Malawi kupita ku South Africa πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡ΏπŸ‡¦

Bye Bye Bus Couches Company ndiyokhayo yodalilika komaso imayenda bwino monga 2 day's pansewu kenako ku South Africa

Ma Bus anthu amayenda Malawi to South Africa

Amene ali ndi passport ntengo ndi 200 thousand kwachοΏ½

Amene alibe passport ntengo ndi 250 thousand kwacha kuchoka ku Malawi kupita ku south AfricaοΏ½

SOUTH AFRICA TO MALAWI
Wa passport ndi R1900
Opanda passport ndi R2500

KATUNDU TIM

ASHAJA TIKAMUONA OSATI KUYEZA PA SKELL AI IFE TILIBE CHOYEZELA ....
MAFUSO MULI OLANDILIDWA ZIKOMO

Alfred Ben

marry Christmas
25/12/2025

marry Christmas

15/03/2025

Mwazuka bwanji...
Maulendo akadalipo

20/11/2024

πŸ˜‡
Ulendo Ochoka dziko la malawi kupita ku South Africa ulipo pa 29 November 2024.......
Bweran muzayende mwadongosolo

16/09/2024
Bye Bye Bus Company offers its deepest condolences to the family, friends, and nation on the passing of Vice President S...
16/06/2024

Bye Bye Bus Company offers its deepest condolences to the family, friends, and nation on the passing of Vice President Saulos Klaus Chilima. May his legacy of courage, leadership, and dedication to public service continue to inspire us all. May he rest in peace.

Rest in peace πŸ’”πŸ’”πŸ’”
11/06/2024

Rest in peace πŸ’”πŸ’”πŸ’”

17/05/2024

Tilipo busy kuseliku ....
Ngat mufuna kuthandizidwa ingotipezani ku number yathuyo

15/11/2023

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Alie Jailos Natoma Jafali, Dalitso January, Adamu KB Kobula Kassmu, Dayton Sabit Wa Amili

20/10/2023

Ife tikafika pa border sitimamiyendesa customer pansi pomwe bus ilipoπŸ‡²πŸ‡Ό

I love you mom kupanda inu sibwezi ndili pano
15/10/2023

I love you mom kupanda inu sibwezi ndili pano

Address

Mwanza
Mwanza

Telephone

+265883820890

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bye Bye Bus Company posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Bye Bye Bus Company:

Share