Maso A Mpemba

Maso A Mpemba Entertainment and development communication. Hot Issues Around Mpemba.

Phungu wa kunyumba ya malamulo mchigawo cha ku mmawa kwa kummwera kwa Blantyre walimbikitsa umodzi potukula derali.Iye w...
07/03/2026

Phungu wa kunyumba ya malamulo mchigawo cha ku mmawa kwa kummwera kwa Blantyre walimbikitsa umodzi potukula derali.
Iye wati anthu akuyenera kugwira ntchito zosiyanasiyana zachitukuko mogwirizana posatengera kusiyana zokonda, kochokera, maonekedwe, udindo, ngakhalenso zipani.
Iyeyu wadzudzuranso anthu kuti achepetse kunyozana mmayankhulidwe, kufalitsa ma uthenga a bodza komanso kuipitsirana Mbiri koma mmalo mwake agwire ntchito yokomera zitukuko za mderali.
Pomwepo walimbikitsanso anthu amderali kutenga gawo pozindikira mavuto omwe alipo mderali ndikukaneneza kwa adindo oyenera.
Pa mapeto pake, walimbikitsanso adindo onse a mderali kuphatikizira oyang'anira chitukuko mmidzi komanso dera lonse kuti atenge gawo lalikulu potsogolera ntchito za chitukuko mderali.

Nkhaniyi yalembedwanso kuchokera pa zomwe, Ambiri Amatero analemba

Mmodzi wa anyamata othamanga mdera linoMervin AkuleAge in Style Mboba🔥🔥
03/03/2026

Mmodzi wa anyamata othamanga mdera lino
Mervin Akule
Age in Style Mboba🔥🔥

13/02/2026


wathu sabata ino

BwandiBwandi... Ndi angati amene mukumudziwa katswiriyu. Munamudziwa bwanji/motani? Ukatswiri wake ndiotani?

   wathu wa sabata inoDzina loimbira: CavistaDzina Lonse: Felix Chola Tsiku lobadwira: 22 December 2002Komwe akukhala: B...
30/01/2026


wathu wa sabata ino

Dzina loimbira: Cavista

Dzina Lonse: Felix Chola

Tsiku lobadwira: 22 December 2002

Komwe akukhala: Blantyre, Chadzunda

Kumudzi kochokera: Blantyre, Mphande VGE

Okwatira: Ayi

Mtundu wa anthu: Yao

Mbiri ya maphunziro: MSCE level

Chamba chomwe amaimba: Any genre kupatula local

Oimba amene amawakonda mdera lino, mdziko muno komanso dziko lonse la pansi: Brika, Lil Kellz, Wiz Baba

Ndalama zomwe amapanga pa mwenzi: Close to 300k

Chakudya chomwe amachikonda: Nsima with nandolo

Mbiri/chomwe chinamulimbikitsa kuyamba kuimba: Kuimba ndi zakumtundu mix achibale angapo ndioimbanso ndiye akamapanga training ndinkangoona and zimandisangalatsa, ndizomwe zinandilimbikitsa nane kulowa studio mix studio'so inali kwathu komko.

Currently, he is set to release a new track on 14 February

   wathu wa sabata inoDzina loimbira: Adolf GidanDzina Lonse: Gideon MalindaTsiku lobadwira: 29 March 2002Komwe akukhala...
24/01/2026


wathu wa sabata ino

Dzina loimbira: Adolf Gidan

Dzina Lonse: Gideon Malinda

Tsiku lobadwira: 29 March 2002

Komwe akukhala: Mpemba

Kumudzi kochokera: Blantyre, Mpemba

Okwatira: Single

Mtundu wa anthu: Yao

Mbiri ya maphunziro: Diploma in public health certificate in tailoring and fashion designing

Chamba chomwe amaimba:

Oimba amene amawakonda mdera lino, mdziko muno komanso dziko lonse la pansi: KiDozi, Chisper-Namadingo, Gattah, Emmie Deebo, Gwamba, Classic, Yanos Central, Zeze- Makhadzi, 6xi9ine, Yo Maps, Diamond on his fashion, Eminem

Ndalama zomwe amapanga pa mwenzi: Depends since now am not financially stable

Chakudya chomwe amachikonda: Polk meat, chips ndiye pakhalenso kamowa wezi

Mbiri/chomwe chinamulimbikitsa kuyamba kuimba: poyamba ndinkakonda kumvera nyimbo kwambiri kenako ndinayamba kumayesera Kulemba zanga koma sindimkapita ku studio, Arthur Minyanga ku ZGSS ndamene anandilimbikitsa kuti ndikalowe studio atapeza ma lyric mu copy mwanga ndipo anawayamikira ngakhale sanali oyimba

Chomwe amafuna atakwaniritsa pa nkhani ya maimbidwe: Kufikira anthu Ambiri Malawi muno ndi kunja, kuwaphunzitsa, kuwasangalasa, ndi kuwadzudzula zomwe zidzaike Mpemba pa map, kunoko ndimafunitsitsa kutazachoka ma artist angapo otchuka mmene ilili Machinjiri, Bangwe, ndi Soche

Nyimbo yake ina: https://youtu.be/oC-XsKNJG0A?si=1_G2poJwF3JXilqK

   WATHU WA SABATA INODzina loimbira: Mr Deng'o Dzina Lonse: Dellen Ching'ombeTsiku lobadwira: 19 November 2000Komwe aku...
16/01/2026


WATHU WA SABATA INO

Dzina loimbira: Mr Deng'o

Dzina Lonse: Dellen Ching'ombe

Tsiku lobadwira: 19 November 2000

Komwe akukhala: Mbayani

Kumudzi kochokera: Malawi, Blantyre, Mpemba

Okwatira: No Idea

Mtundu wa anthu: Yao and Chewa

Mbiri ya maphunziro:Form 4, Salima Community Day Secondary School

Oimba amene amamukonda mdera lino, mdziko muno komanso dziko lonse la pansi: M Rich m'dera lino ndipo dziko muno Namadingo, kunja Tekno

Ndalama zomwe amapanga pa mwenzi: Sizambiri kwenikweni malingana ndi pomwe ndili

Chakudya chomwe amachikonda: Nsima ya kondole mix chapamwamba komanso mpunga wa ma ofozi

Mbiri/chomwe chinamulimbikitsa kuyamba kuimba: ndinayamba kuimba chifukwa ndimakonda kumvera nyimbo, weziwezi ndinayamba kumayesera pandekha mpakana kufikira mu chaka cha 2018 pomwe ndinakalowa ku studio, Sub Mart Records. Weziwezi ndikumaphusha kufikira pomwe ndilipa

Chomwe amafuna atakwaniritsa pa nkhani ya maimbidwe: ndimafuna ndidzafikire level Yoti aliyense azadziwe luso langa la maimbidwe muno M'malawi komanso maiko akunja

   WATHU WA SABATA INODzina loimbira: KiDoziDzina Lonse: Fletcher Emmanuel SailesTsiku lobadwira: 23 October 2000Komwe a...
09/01/2026



WATHU WA SABATA INO

Dzina loimbira: KiDozi

Dzina Lonse: Fletcher Emmanuel Sailes

Tsiku lobadwira: 23 October 2000

Komwe akukhala: Ntaunimu😆

Kumudzi kochokera: Nsanganiza Village, Mpemba, Blantyre.

Okwatira: Kaya, mwinanso ndili single😖

Mtundu wa anthu: 4 in one-Yao, Lhomwe, Mang'anja and chewa😎😎

Mbiri ya maphunziro: Graduated from University of Malawi formerly known as Chancellor College, Media for Development programme.

Oimba amene amamukonda mdera lino, mdziko muno komanso dziko lonse la pansi: Jasper, Piksy ndi Adekunle Gold.

Ndalama zomwe amapanga pa mwenzi: Zochepa😔😔

Chakudya chomwe amachikonda: Nsima and Pork/beans with masamba otendera.

Mbiri ndi chomwe chinamulimbikitsa kuyamba kuimba: ndinkakonda kumvera komanso kuonera nyimbo ndiye zimandipanga inspire, then we started playing local drums with my childhood friends and writing lyrics when I was in standard 3 till when I started studio recording in 2018.

Chomwe amafuna atakwaniritsa pa nkhani ya maimbidwe: kufikira anthu Ambiri mmene ndingathere.

Nyimbo yatsopano: https://youtu.be/anyiD7hUO-0?si=0HZ6AEHhoJAu8p2t

20/11/2025

Tatchuran munthu mmodzi wa luso ticheze naye mawali😎😎

20/11/2025

Hello a Maso nonse pano. Tiyeni ku WhatsApp tikacheze kumeneku😎😎
Hit the link here

19/10/2025

Anthu inu, oyimba anuwa mukumawamvera koma?? TATCHURAN OIMBA MMODZI KWANUKO, NDINYIMBO ZITATU ZOMWE ANAIMBA..

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Maso A Mpemba posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share